Yesaya 39:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 ‘Ena mwa ana ako ochokera mwa iwe, amene iweyo udzakhale bambo wawo, nawonso adzatengedwa+ ndipo adzakhala nduna za panyumba+ ya mfumu ya ku Babulo.’”+ Yeremiya 52:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kenako anayamba kulankhula naye zinthu zabwino, ndipo anakweza ufumu wake kuposa mafumu ena amene anali naye limodzi ku Babulo.+
7 ‘Ena mwa ana ako ochokera mwa iwe, amene iweyo udzakhale bambo wawo, nawonso adzatengedwa+ ndipo adzakhala nduna za panyumba+ ya mfumu ya ku Babulo.’”+
32 Kenako anayamba kulankhula naye zinthu zabwino, ndipo anakweza ufumu wake kuposa mafumu ena amene anali naye limodzi ku Babulo.+