2 Mafumu 20:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Ena mwa ana ako ochokera mwa iwe, amene iweyo udzakhale bambo wawo, nawonso adzatengedwa+ ndipo adzakhala nduna+ za panyumba ya mfumu ya ku Babulo.”’”+
18 “Ena mwa ana ako ochokera mwa iwe, amene iweyo udzakhale bambo wawo, nawonso adzatengedwa+ ndipo adzakhala nduna+ za panyumba ya mfumu ya ku Babulo.”’”+