Danieli 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo mfumu inayamba kulankhula nawo ndipo pa ana onsewo, palibe aliyense amene anali ngati Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya.+ Chotero ana amenewa anapitiriza kutumikira mfumu.+ Danieli 2:49 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ kuti akhale oyang’anira chigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli anali kutumikira m’nyumba ya mfumu.+
19 Pamenepo mfumu inayamba kulankhula nawo ndipo pa ana onsewo, palibe aliyense amene anali ngati Danieli, Hananiya, Misayeli ndi Azariya.+ Chotero ana amenewa anapitiriza kutumikira mfumu.+
49 Ndipo Danieli anapempha mfumu kuti iike Sadirake, Mesake ndi Abedinego+ kuti akhale oyang’anira chigawo cha Babulo, ndipo mfumuyo inawaikadi. Koma Danieli anali kutumikira m’nyumba ya mfumu.+