Danieli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakati pa anawo panali ana ena a ku Yuda. Mayina awo anali Danieli,+ Hananiya, Misayeli ndi Azariya,+
6 Pakati pa anawo panali ana ena a ku Yuda. Mayina awo anali Danieli,+ Hananiya, Misayeli ndi Azariya,+