Danieli 2:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 Pa chifukwa chimenechi, mfumu inamukweza pa udindo Danieli+ ndipo inamupatsa mphatso zambiri. Inamuikanso kukhala wolamulira chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso wamkulu wa akuluakulu a boma* oyang’anira amuna onse anzeru a m’Babulo. Danieli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anabweretsa Danieli kwa mfumu, ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Kodi iwe ndiwe Danieli, mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda+ ndi bambo anga mfumu?+ Danieli 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+
48 Pa chifukwa chimenechi, mfumu inamukweza pa udindo Danieli+ ndipo inamupatsa mphatso zambiri. Inamuikanso kukhala wolamulira chigawo chonse cha Babulo+ ndiponso wamkulu wa akuluakulu a boma* oyang’anira amuna onse anzeru a m’Babulo.
13 Choncho anabweretsa Danieli kwa mfumu, ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Kodi iwe ndiwe Danieli, mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda+ ndi bambo anga mfumu?+
29 Pamenepo Belisazara analamula kuti Danieli amuveke zovala zofiirira ndi mkanda wagolide m’khosi mwake, ndipo analengeza kuti Danieli akhala wolamulira wachitatu mu ufumuwo.+