Danieli 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakati pa anawo panali ana ena a ku Yuda. Mayina awo anali Danieli,+ Hananiya, Misayeli ndi Azariya,+ Danieli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu ndi kuiuza kuti: “Ndapeza mwamuna wamphamvu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo+ ku Yuda yemwe angamasulire maloto anu mfumu.” Danieli 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli,+ mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sanakumvereni mfumu komanso sanamvere lamulo limene munasainira ndipo akupemphera katatu pa tsiku.”+
6 Pakati pa anawo panali ana ena a ku Yuda. Mayina awo anali Danieli,+ Hananiya, Misayeli ndi Azariya,+
25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu ndi kuiuza kuti: “Ndapeza mwamuna wamphamvu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo+ ku Yuda yemwe angamasulire maloto anu mfumu.”
13 Nthawi yomweyo iwo anauza mfumuyo kuti: “Danieli,+ mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda,+ sanakumvereni mfumu komanso sanamvere lamulo limene munasainira ndipo akupemphera katatu pa tsiku.”+