Danieli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu ndi kuiuza kuti: “Ndapeza mwamuna wamphamvu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo+ ku Yuda yemwe angamasulire maloto anu mfumu.” Danieli 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Choncho anabweretsa Danieli kwa mfumu, ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Kodi iwe ndiwe Danieli, mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda+ ndi bambo anga mfumu?+
25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu ndi kuiuza kuti: “Ndapeza mwamuna wamphamvu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo+ ku Yuda yemwe angamasulire maloto anu mfumu.”
13 Choncho anabweretsa Danieli kwa mfumu, ndipo mfumuyo inamufunsa kuti: “Kodi iwe ndiwe Danieli, mmodzi wa anthu amene anatengedwa ukapolo ku Yuda+ ndi bambo anga mfumu?+