2 Mafumu 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Kenako Farao Neko+ anamanga+ Yehoahazi ku Ribila+ m’dziko la Hamati, kuti asalamulirenso ku Yerusalemu. Ndiyeno Farao Neko analamula+ dzikolo kuti lim’patse matalente 100 a siliva+ ndi talente imodzi ya golide.+ Yeremiya 52:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero mfumu ya Babulo inapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, iye akuona.+ Inaphanso akalonga onse a ku Yuda.+ Yeremiya 52:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga anthuwa n’kupita nawo ku Ribila kwa mfumu ya Babulo.+
33 Kenako Farao Neko+ anamanga+ Yehoahazi ku Ribila+ m’dziko la Hamati, kuti asalamulirenso ku Yerusalemu. Ndiyeno Farao Neko analamula+ dzikolo kuti lim’patse matalente 100 a siliva+ ndi talente imodzi ya golide.+
10 Zitatero mfumu ya Babulo inapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, iye akuona.+ Inaphanso akalonga onse a ku Yuda.+
26 Choncho, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga anthuwa n’kupita nawo ku Ribila kwa mfumu ya Babulo.+