2 Mafumu 25:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako Akasidiwo anagwira mfumuyo+ n’kupita nayo ku Ribila+ kwa mfumu ya Babulo, kuti akaiuze chigamulo chake. Yeremiya 39:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linawathamangitsa+ ndipo Zedekiya anamupeza m’chipululu cha Yeriko.+ Atamugwira, anamutenga ndi kupita naye kwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo ku Ribila,+ m’dziko la Hamati,+ kuti Nebukadirezara akamuweruze.+ Yeremiya 52:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Zitatero mfumu ya Babulo inapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, iye akuona.+ Inaphanso akalonga onse a ku Yuda.+ Yeremiya 52:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga anthuwa n’kupita nawo ku Ribila kwa mfumu ya Babulo.+
6 Kenako Akasidiwo anagwira mfumuyo+ n’kupita nayo ku Ribila+ kwa mfumu ya Babulo, kuti akaiuze chigamulo chake.
5 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linawathamangitsa+ ndipo Zedekiya anamupeza m’chipululu cha Yeriko.+ Atamugwira, anamutenga ndi kupita naye kwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo ku Ribila,+ m’dziko la Hamati,+ kuti Nebukadirezara akamuweruze.+
10 Zitatero mfumu ya Babulo inapha ana aamuna a Zedekiya ku Ribila, iye akuona.+ Inaphanso akalonga onse a ku Yuda.+
26 Choncho, Nebuzaradani+ mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga anthuwa n’kupita nawo ku Ribila kwa mfumu ya Babulo.+