Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 6:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Iwe mwana wamkazi wa anthu anga, vala chiguduli*+ ndi kuvimvinizika m’phulusa.+ Lira ngati kuti ukulira maliro a mwana wamwamuna mmodzi yekhayo. Lira mowawidwa mtima+ chifukwa wofunkha adzatiukira modzidzimutsa.+

  • Ezekieli 27:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Iwo adzakulirira mofuula ndi mowawidwa mtima.+ Adzadzithira dothi kumutu+ ndi kugubuduzika paphulusa.+

  • Yona 3:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Uthengawo utafika kwa mfumu ya Nineve,+ mfumuyo inanyamuka pampando wake wachifumu ndi kuvula chovala chake chachifumu. Ndiyeno inavala chiguduli ndi kukhala paphulusa.+

  • Yona 3:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Munthu aliyense komanso ziweto zivale chiguduli. Afuulire Mulungu ndi mphamvu zawo zonse, ndipo aliyense asiye njira zake zoipa+ ndi zinthu zonse zachiwawa zimene amachita.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena