Yesaya 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Sambani,+ dziyeretseni.+ Chotsani zochita zanu zoipa pamaso panga.+ Lekani kuchita zoipa.+ Ezekieli 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “‘Munthu woipa akabwerera, kusiya machimo ake onse amene anali kuchita+ ndipo akasunga malamulo anga onse n’kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+ Yoweli 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wanu wonse.+ Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokuwa.+ Mateyu 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyetu mubale zipatso zosonyeza kulapa.+ Machitidwe 3:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 “Chotero lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa+ zibwere kuchokera kwa Yehova.
21 “‘Munthu woipa akabwerera, kusiya machimo ake onse amene anali kuchita+ ndipo akasunga malamulo anga onse n’kuchita zinthu motsatira malamulo ndiponso mwachilungamo,+ adzakhalabe ndi moyo. Sadzafa ayi.+
12 Yehova wanenanso kuti, “Tsopano bwererani kwa ine ndi mtima wanu wonse.+ Salani kudya,+ lirani momvetsa chisoni ndiponso mokuwa.+
19 “Chotero lapani+ ndi kutembenuka+ kuti machimo anu afafanizidwe,+ ndiponso kuti nyengo zotsitsimutsa+ zibwere kuchokera kwa Yehova.