Yohane 10:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ine ndine m’busa wabwino.+ M’busa wabwino amataya moyo wake chifukwa cha nkhosa.+ Aroma 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pakuti n’chapatali kuti munthu wina afere munthu wolungama.+ Zoonadi, mwina wina angalimbe mtima kufera+ munthu wabwino.+ Aefeso 5:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 ndipo yendanibe m’chikondi,+ monganso Khristu anakukondani+ n’kudzipereka yekha chifukwa cha inu. Iye anadzipereka yekha monga chopereka+ ndiponso monga nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+ 1 Yohane 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Tadziwa chikondi+ chifukwa chakuti iye anapereka moyo wake chifukwa cha ife,+ ndipo ifenso tiyenera kupereka moyo wathu chifukwa cha abale athu.+
7 Pakuti n’chapatali kuti munthu wina afere munthu wolungama.+ Zoonadi, mwina wina angalimbe mtima kufera+ munthu wabwino.+
2 ndipo yendanibe m’chikondi,+ monganso Khristu anakukondani+ n’kudzipereka yekha chifukwa cha inu. Iye anadzipereka yekha monga chopereka+ ndiponso monga nsembe yafungo lokoma kwa Mulungu.+
16 Tadziwa chikondi+ chifukwa chakuti iye anapereka moyo wake chifukwa cha ife,+ ndipo ifenso tiyenera kupereka moyo wathu chifukwa cha abale athu.+