Salimo 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Uchimo ukulankhula mumtima mwa munthu woipa.+Maso ake saona chifukwa choopera Mulungu.+ Salimo 53:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+ Yohane 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma adzachita zimenezi chifukwa sanadziwe Atate kapena ine.+
4 Kodi palibe aliyense wozindikira mwa anthu ochita zopweteka anzawowa,+Amene akudya anthu anga ngati chakudya?+Iwo sanaitane pa Yehova.+