Yohane 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo iwo anati: “Atate wako ali kuti?” Yesu anayankha kuti: “Inu simukundidziwa ine kapena Atate wanga.+ Mukanandidziwa ine, mukanadziwanso Atate wanga.”+ Yohane 15:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha dzina langa, chifukwa amene anandituma ine sakumudziwa.+ Aroma 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti ndikuwachitira umboni kuti ndi odzipereka+ potumikira Mulungu, koma samudziwa molondola.+ 1 Akorinto 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Palibe wolamulira+ ndi mmodzi yemwe wa nthawi* ino amene anadziwa+ nzeru imeneyi, chifukwa ngati anali kuidziwa sakanapachika+ Ambuye waulemereroyo.
19 Pamenepo iwo anati: “Atate wako ali kuti?” Yesu anayankha kuti: “Inu simukundidziwa ine kapena Atate wanga.+ Mukanandidziwa ine, mukanadziwanso Atate wanga.”+
21 Koma adzakuchitirani zonsezi chifukwa cha dzina langa, chifukwa amene anandituma ine sakumudziwa.+
8 Palibe wolamulira+ ndi mmodzi yemwe wa nthawi* ino amene anadziwa+ nzeru imeneyi, chifukwa ngati anali kuidziwa sakanapachika+ Ambuye waulemereroyo.