Genesis 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abulahamu anayankha kuti: “Ndachita zimenezi poganiza kuti, ‘Ndithu anthu a kuno saopa Mulungu,+ andipha ndithu chifukwa cha mkazi wangayu.’+ Aroma 3:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Maso awo saona chifukwa choopera Mulungu.”+
11 Abulahamu anayankha kuti: “Ndachita zimenezi poganiza kuti, ‘Ndithu anthu a kuno saopa Mulungu,+ andipha ndithu chifukwa cha mkazi wangayu.’+