Genesis 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abulahamu anayankha kuti: “Ndachita zimenezi poganiza kuti, ‘Ndithu anthu a kuno saopa Mulungu,+ andipha ndithu chifukwa cha mkazi wangayu.’+ Salimo 36:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Uchimo ukulankhula mumtima mwa munthu woipa.+Maso ake saona chifukwa choopera Mulungu.+ Salimo 112:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 112 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Wodala ndi munthu woopa Yehova,+ב [Behth]Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+ Miyambo 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi,+ ndipo chifukwa choopa Yehova munthu amapatuka pa choipa.+
11 Abulahamu anayankha kuti: “Ndachita zimenezi poganiza kuti, ‘Ndithu anthu a kuno saopa Mulungu,+ andipha ndithu chifukwa cha mkazi wangayu.’+
112 Tamandani Ya, anthu inu!+ א [ʼAʹleph]Wodala ndi munthu woopa Yehova,+ב [Behth]Munthu amene amasangalala kwambiri+ ndi malamulo ake.+
6 Cholakwa chimaphimbika ndi kukoma mtima kosatha ndiponso choonadi,+ ndipo chifukwa choopa Yehova munthu amapatuka pa choipa.+