1 Samueli 18:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuyambira tsiku limenelo, Sauli anayamba kuyang’ana Davide ndi diso loipa.+ 1 Samueli 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Zitatero, Sauli anachita mantha+ ndi Davide chifukwa Yehova anali ndi Davideyo,+ koma Sauliyo anali atam’chokera.+ 1 Samueli 20:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+ Salimo 37:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Woipa akukonzera chiwembu munthu wolungama,+Ndipo akumukukutira mano.+
12 Zitatero, Sauli anachita mantha+ ndi Davide chifukwa Yehova anali ndi Davideyo,+ koma Sauliyo anali atam’chokera.+
33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+