Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 20:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Atatero, Sauli anaponya mkondo wake kuti amulase.+ Pamenepo Yonatani anadziwa kuti bambo ake anatsimikiza mtima kupha Davide.+

  • 1 Samueli 21:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Pamenepo Davide ananyamuka tsiku limenelo, ndipo anapitiriza kuthawa+ chifukwa choopa Sauli. Patapita nthawi anafika kwa Akisi mfumu ya Gati.+

  • Miyambo 27:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mkwiyo umasefukira ndipo ukali ndi wankhanza,+ koma nsanje ndani angaipirire?+

  • 1 Timoteyo 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 munthu ameneyo ndi wodzitukumula ndiponso wonyada,+ ndipo samvetsa kanthu kalikonse.+ M’malomwake, amakonda kukangana ndi anthu ndiponso kutsutsana pa mawu.+ Zimenezi zimayambitsa kaduka,+ mikangano, kunenerana mawu achipongwe,+ ndiponso kuganizirana zoipa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena