Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 11:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 M’dziko la ana a Isiraeli, palibe Aanaki amene anatsalamo,+ kupatulapo okhala ku Gaza,+ ku Gati+ ndi ku Asidodi.+

  • 1 Samueli 5:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Chotero anatumiza uthenga ndi kusonkhanitsa olamulira onse ogwirizana a Afilisiti ku Asidodi ndi kuwauza kuti: “Tichite nalo chiyani likasa la Mulungu wa Isiraeli?” Pamapeto pake iwo anati: “Likasa limeneli la Mulungu wa Isiraeli tilitumize kumzinda wa Gati.”+ Choncho anapititsa likasa la Mulungu wa Isiraeli kumeneko atayenda nalo mozungulira.

  • 1 Samueli 17:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno kumsasa wa Afilisiti kunatuluka ngwazi, dzina lake Goliyati,+ wa ku Gati.+ Iye anali wamtali mikono 6 ndi chikhatho chimodzi.*+

  • 1 Samueli 27:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Choncho Davide pamodzi ndi amuna 600+ amene anali kuyenda naye ananyamuka ndi kupita kwa Akisi+ mfumu ya Gati, mwana wa Maoki.

  • 1 Mafumu 2:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Pamapeto pa zaka zitatu, akapolo awiri+ a Simeyi anathawira kwa Akisi+ mwana wa Maaka, mfumu ya Gati.+ Kenako anthu anabwera kudzauza Simeyi kuti: “Tamvera! Akapolo ako ali ku Gati.”

  • 2 Mafumu 12:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Panthawi imeneyo Hazaeli+ mfumu ya Siriya anapita kukamenyana ndi mzinda wa Gati+ n’kuulanda. Kenako Hazaeli anatsimikiza zopita*+ kukaukira Yerusalemu.+

  • Salimo 56:kam
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • Kwa wotsogolera nyimbo pa “Nkhunda Yosanena Kanthu” pakati pa okhala kutali. Salimo la Davide. Mikitamu.* Pa nthawi imene Afilisiti anamugwira ku Gati.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena