Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Kuchokera ku Ekironi kulowera chakumadzulo, malo onse amene ali m’mphepete mwa Asidodi ndi midzi yake.

  • 2 Mbiri 26:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Iye anapita kukamenyana ndi Afilisiti+ ndipo anagumula mpanda wa ku Gati,+ wa ku Yabine+ ndi wa ku Asidodi.+ Kenako anamanga mizinda m’chigawo cha Asidodi+ ndiponso pakati pa Afilisiti.

  • Nehemiya 13:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Komanso ndinaona kuti Ayuda ena anali atakwatira+ akazi achiasidodi,+ achiamoni ndi achimowabu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena