2 Samueli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa,+ ndipo anawalanda mzinda wa Metege-ama. 2 Mbiri 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chotero Yehova anachititsa Afilisiti+ ndi Aluya+ amene anali pafupi ndi Aitiyopiya+ kuukira Yehoramu.+ Yesaya 14:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Usasangalale+ iwe Filisitiya,+ kapena aliyense wokhala mwa iwe chifukwa chakuti ndodo ya amene anali kukumenya yathyoka.+ Pakuti pamuzu wa njokayo+ padzaphuka njoka yapoizoni,+ ndipo chipatso chake chidzakhala njoka yothamanga, yaululu wamoto.+
16 Chotero Yehova anachititsa Afilisiti+ ndi Aluya+ amene anali pafupi ndi Aitiyopiya+ kuukira Yehoramu.+
29 “Usasangalale+ iwe Filisitiya,+ kapena aliyense wokhala mwa iwe chifukwa chakuti ndodo ya amene anali kukumenya yathyoka.+ Pakuti pamuzu wa njokayo+ padzaphuka njoka yapoizoni,+ ndipo chipatso chake chidzakhala njoka yothamanga, yaululu wamoto.+