2 Mafumu 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mfumuyo inamva kuti Tirihaka mfumu ya Itiyopiya wabwera kudzamenyana nayo. Choncho inatumizanso amithenga+ kwa Hezekiya n’kuwauza kuti: 2 Mbiri 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anabwera ndi magaleta 1,200+ ndi amuna okwera pamahatchi 60,000. Anabweranso ndi anthu osawerengeka+ kuchokera ku Iguputo. Anthuwo anali Alibiya,+ Asuki ndi Aitiyopiya.+ 2 Mbiri 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Atatero, Yehova anagonjetsa+ Aitiyopiyawo pamaso pa Asa ndi Ayuda, ndipo Aitiyopiyawo anayamba kuthawa.
9 Mfumuyo inamva kuti Tirihaka mfumu ya Itiyopiya wabwera kudzamenyana nayo. Choncho inatumizanso amithenga+ kwa Hezekiya n’kuwauza kuti:
3 Anabwera ndi magaleta 1,200+ ndi amuna okwera pamahatchi 60,000. Anabweranso ndi anthu osawerengeka+ kuchokera ku Iguputo. Anthuwo anali Alibiya,+ Asuki ndi Aitiyopiya.+
12 Atatero, Yehova anagonjetsa+ Aitiyopiyawo pamaso pa Asa ndi Ayuda, ndipo Aitiyopiyawo anayamba kuthawa.