2 Mbiri 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pambuyo pake Zera Mwitiyopiya+ anabwera kudzamenyana nawo ali ndi gulu lankhondo la asilikali 1,000,000+ ndi magaleta 300, ndipo anafika ku Maresha.+ 2 Mbiri 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kodi Aitiyopiya+ ndi Alibiya+ sanali gulu lankhondo lalikulu, la anthu ambiri, magaleta ambiri, ndi okwera pamahatchi ambirinso?+ Chifukwa chakuti munadalira Yehova, kodi iye sanawapereke m’manja mwanu?+
9 Pambuyo pake Zera Mwitiyopiya+ anabwera kudzamenyana nawo ali ndi gulu lankhondo la asilikali 1,000,000+ ndi magaleta 300, ndipo anafika ku Maresha.+
8 Kodi Aitiyopiya+ ndi Alibiya+ sanali gulu lankhondo lalikulu, la anthu ambiri, magaleta ambiri, ndi okwera pamahatchi ambirinso?+ Chifukwa chakuti munadalira Yehova, kodi iye sanawapereke m’manja mwanu?+