2 Mafumu 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mfumuyo inamva kuti Tirihaka mfumu ya Itiyopiya wabwera kudzamenyana nayo. Choncho inatumizanso amithenga+ kwa Hezekiya n’kuwauza kuti: Machitidwe 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Choncho, ananyamuka ndi kupita. Kumeneko anakumana ndi nduna+ ya ku Itiyopiya,+ munthu waulamuliro pansi pa Kandake, mfumukazi ya Itiyopiya. Iye anali woyang’anira chuma chonse cha mfumukaziyo. Iyeyu anapita ku Yerusalemu kukapembedza Mulungu,+
9 Mfumuyo inamva kuti Tirihaka mfumu ya Itiyopiya wabwera kudzamenyana nayo. Choncho inatumizanso amithenga+ kwa Hezekiya n’kuwauza kuti:
27 Choncho, ananyamuka ndi kupita. Kumeneko anakumana ndi nduna+ ya ku Itiyopiya,+ munthu waulamuliro pansi pa Kandake, mfumukazi ya Itiyopiya. Iye anali woyang’anira chuma chonse cha mfumukaziyo. Iyeyu anapita ku Yerusalemu kukapembedza Mulungu,+