2 Mbiri 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anabwera ndi magaleta 1,200+ ndi amuna okwera pamahatchi 60,000. Anabweranso ndi anthu osawerengeka+ kuchokera ku Iguputo. Anthuwo anali Alibiya,+ Asuki ndi Aitiyopiya.+
3 Anabwera ndi magaleta 1,200+ ndi amuna okwera pamahatchi 60,000. Anabweranso ndi anthu osawerengeka+ kuchokera ku Iguputo. Anthuwo anali Alibiya,+ Asuki ndi Aitiyopiya.+