Obadiya 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Iwe sunayenera kumangoonerera mosangalala pa tsiku limene m’bale wako anakumana ndi tsoka.+ Sunayenera kusangalala pa tsiku limene ana a Yuda anali kuwonongedwa.+ Sunayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene iwo anamva zowawa.
12 “Iwe sunayenera kumangoonerera mosangalala pa tsiku limene m’bale wako anakumana ndi tsoka.+ Sunayenera kusangalala pa tsiku limene ana a Yuda anali kuwonongedwa.+ Sunayeneranso kulankhula modzitama pa tsiku limene iwo anamva zowawa.