Yoswa 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dziko limene latsala ndi ili:+ Madera onse a Afilisiti+ ndi madera onse a Agesuri.+ 2 Samueli 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Davide anapha Afilisiti+ ndi kuwagonjetsa,+ ndipo anawalanda mzinda wa Metege-ama.