Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 6:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Uchipange motere: M’litali chikhale mikono*+ 300, m’lifupi mikono 50, ndipo kutalika kwake kuyambira pansi mpaka pamwamba chikhale mikono 30.

  • Deuteronomo 3:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Mwa Arefai+ onse, Ogi yekha mfumu ya Basana ndi amene anali atatsala. Chithatha chimene anaikapo mtembo wake chinali chachitsulo. Kodi si chija chili ku Raba+ wa ana a Aamoni? N’chachitali mikono* 9, ndipo m’lifupi mwake mikono inayi, kutsatira muyezo wodziwika.

  • 2 Samueli 21:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Panabukanso nkhondo ina ku Gati,+ pa nthawi imene kunali munthu wa msinkhu waukulu modabwitsa. Iye anali ndi zala 6 kudzanja lililonse ndiponso zala 6 kuphazi lililonse, moti anali ndi zala 24 zonse pamodzi. Ameneyunso anali mmodzi mwa mbadwa za Arefai.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena