2 Samueli 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero, Isibi-benobi mmodzi wa mbadwa za Arefai,+ amene anali ndi mkondo wamkuwa wolemera+ masekeli 300,* amenenso anali ndi lupanga latsopano m’chiuno mwake, anaganiza zoti aphe Davide.
16 Zitatero, Isibi-benobi mmodzi wa mbadwa za Arefai,+ amene anali ndi mkondo wamkuwa wolemera+ masekeli 300,* amenenso anali ndi lupanga latsopano m’chiuno mwake, anaganiza zoti aphe Davide.