2 Samueli 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero, Isibi-benobi, mbadwa ya Arefai+ amene anali ndi mkondo wakopa wolemera makilogalamu pafupifupi atatu ndi hafu*+ komanso lupanga latsopano, ankafuna kupha Davide. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:16 Nsanja ya Olonda,1/15/2013, ptsa. 30-31
16 Zitatero, Isibi-benobi, mbadwa ya Arefai+ amene anali ndi mkondo wakopa wolemera makilogalamu pafupifupi atatu ndi hafu*+ komanso lupanga latsopano, ankafuna kupha Davide.