2 Samueli 21:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zitatero, Isibi-benobi mmodzi wa mbadwa za Arefai,+ amene anali ndi mkondo wamkuwa wolemera+ masekeli 300,* amenenso anali ndi lupanga latsopano m’chiuno mwake, anaganiza zoti aphe Davide. 2 Samueli Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 21:16 Nsanja ya Olonda,1/15/2013, ptsa. 30-31
16 Zitatero, Isibi-benobi mmodzi wa mbadwa za Arefai,+ amene anali ndi mkondo wamkuwa wolemera+ masekeli 300,* amenenso anali ndi lupanga latsopano m’chiuno mwake, anaganiza zoti aphe Davide.