1 Samueli 21:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo Davide ananyamuka tsiku limenelo, ndipo anapitiriza kuthawa+ chifukwa choopa Sauli. Patapita nthawi anafika kwa Akisi mfumu ya Gati.+ 1 Samueli 27:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Akisi anakhulupirira+ Davide, ndipo mumtima mwake anati: “Mosakayikira, Davide wakhala fungo lonunkha kwa anthu akwawo Aisiraeli,+ ndipo iye akhala mtumiki wanga mpaka kalekale.”
10 Pamenepo Davide ananyamuka tsiku limenelo, ndipo anapitiriza kuthawa+ chifukwa choopa Sauli. Patapita nthawi anafika kwa Akisi mfumu ya Gati.+
12 Akisi anakhulupirira+ Davide, ndipo mumtima mwake anati: “Mosakayikira, Davide wakhala fungo lonunkha kwa anthu akwawo Aisiraeli,+ ndipo iye akhala mtumiki wanga mpaka kalekale.”