Yoswa 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 M’dziko la ana a Isiraeli, palibe Aanaki amene anatsalamo,+ kupatulapo okhala ku Gaza,+ ku Gati+ ndi ku Asidodi.+ 2 Samueli 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Anthu anayi amenewa anali mbadwa za Arefai ku Gati.+ Iwo anaphedwa ndi dzanja la Davide ndi la atumiki ake.+ 1 Mbiri 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anthu amenewa anali mbadwa za Arefai+ ku Gati.+ Iwo anaphedwa+ ndi dzanja la Davide ndi la atumiki ake.
22 M’dziko la ana a Isiraeli, palibe Aanaki amene anatsalamo,+ kupatulapo okhala ku Gaza,+ ku Gati+ ndi ku Asidodi.+
22 Anthu anayi amenewa anali mbadwa za Arefai ku Gati.+ Iwo anaphedwa ndi dzanja la Davide ndi la atumiki ake.+
8 Anthu amenewa anali mbadwa za Arefai+ ku Gati.+ Iwo anaphedwa+ ndi dzanja la Davide ndi la atumiki ake.