-
Ezekieli 32:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Kodi amenewa sadzagona limodzi ndi anthu amphamvu+ amene anaphedwa pakati pa anthu osadulidwa? Kodi sadzagona limodzi ndi anthu amene anatsikira ku Manda limodzi ndi zida zawo zankhondo? Mitu yawo idzatsamira malupanga awo ndipo mafupa awo adzalangidwa chifukwa cha zolakwa zawo,+ chifukwa anthu amphamvuwo anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.+
-