Ezekieli 32:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Manda a Asuri ali pakatikati pa dzenje+ ndipo khamu lake lonse lazungulira manda akewo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga chifukwa anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.
23 Manda a Asuri ali pakatikati pa dzenje+ ndipo khamu lake lonse lazungulira manda akewo. Onsewo anaphedwa ndi lupanga chifukwa anachititsa mantha anthu m’dziko la anthu amoyo.