2 Samueli 10:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Chita zinthu mwamphamvu, ndipo tisonyeze kulimba mtima+ chifukwa cha anthu athu, ndiponso chifukwa cha mizinda ya Mulungu wathu.+ Yehova adzachita zimene zili zabwino m’maso mwake.”+ Salimo 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mulungu woona Ndiye amandilimbitsa,*+Ndipo adzasalaza njira yanga.+ Salimo 108:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndi thandizo la Mulungu, tidzalandira mphamvu,+Ndipo Mulungu adzapondereza adani athu.+
12 Chita zinthu mwamphamvu, ndipo tisonyeze kulimba mtima+ chifukwa cha anthu athu, ndiponso chifukwa cha mizinda ya Mulungu wathu.+ Yehova adzachita zimene zili zabwino m’maso mwake.”+
32 Mulungu woona Ndiye amandilimbitsa,*+Ndipo adzasalaza njira yanga.+ Salimo 108:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndi thandizo la Mulungu, tidzalandira mphamvu,+Ndipo Mulungu adzapondereza adani athu.+