Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Oponya mivi ndi uta mwaluso agwidwa ndi mantha,+

      Koma olefuka apeza mphamvu zochuluka.+

  • 2 Samueli 22:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Inu mudzandiveka mphamvu kuti ndithe kumenya nkhondo.+

      Mudzakomola ondiukira.+

  • Salimo 18:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Mulungu woona Ndiye amandilimbitsa,*+

      Ndipo adzasalaza njira yanga.+

  • Salimo 84:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Mphamvu zawo zidzapitiriza kuwonjezeka pamene akuyenda.+

      Aliyense wa iwo amaonekera kwa Mulungu mu Ziyoni.+

  • Yesaya 40:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Iye amapereka mphamvu kwa munthu wotopa,+ ndipo wofooka amam’patsa nyonga zochuluka.+

  • 2 Akorinto 4:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komabe, tili ndi chuma+ chimenechi m’zonyamulira+ zoumbidwa ndi dothi,+ kuti mphamvu+ yoposa yachibadwa ichokere kwa Mulungu,+ osati kwa ife.+

  • Afilipi 4:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pa zinthu zonse, ndimapeza mphamvu kuchokera kwa iye amene amandipatsa mphamvu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena