Salimo 37:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Lupanga lawo lidzalowa mumtima mwawo,+Ndipo mauta awo adzathyoka.+ Salimo 76:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kumeneko wathyola mivi yoyaka moto,+Wathyola chishango, lupanga ndi zida zankhondo.+ [Seʹlah.]