Salimo 8:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndimaganiza kuti: Munthu+ ndani kuti muzimuganizira,+Ndipo mwana wa munthu wochokera kufumbi ndani kuti muzimusamalira?+ Yesaya 64:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+ 1 Akorinto 15:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi fumbi.+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+
4 Ndimaganiza kuti: Munthu+ ndani kuti muzimuganizira,+Ndipo mwana wa munthu wochokera kufumbi ndani kuti muzimusamalira?+
8 Komatu inu Yehova, inu ndinu Atate wathu.+ Ife ndife dongo+ ndipo inu ndinu Wotiumba.+ Tonsefe ndife ntchito ya manja anu.+
47 Munthu woyambayo anachokera padziko lapansi ndipo anapangidwa ndi fumbi.+ Wachiwiriyo anachokera kumwamba.+