Machitidwe 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli. 1 Atesalonika 4:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Akufunanso kuti aliyense wa inu akhale woyera mwa kudziwa kulamulira thupi lake+ m’njira yoyera+ kuti mukhale olemekezeka pamaso pa Mulungu,
15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli.
4 Akufunanso kuti aliyense wa inu akhale woyera mwa kudziwa kulamulira thupi lake+ m’njira yoyera+ kuti mukhale olemekezeka pamaso pa Mulungu,