Aroma 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kudzera mwa iyeyu, tinalandira kukoma mtima+ kwakukulu ndiponso ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti mitundu yonse ikhale yomvera mwa chikhulupiriro+ chifukwa cha dzina lake. Agalatiya 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma iwo ataona kuti ndapatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mmene Petulo anapatsidwira ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa,+ 1 Timoteyo 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona,+ sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndikhale mphunzitsi wophunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro+ ndi choonadi.
5 Kudzera mwa iyeyu, tinalandira kukoma mtima+ kwakukulu ndiponso ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti mitundu yonse ikhale yomvera mwa chikhulupiriro+ chifukwa cha dzina lake.
7 Koma iwo ataona kuti ndapatsidwa+ ntchito yolalikira uthenga wabwino kwa anthu osadulidwa,+ mmene Petulo anapatsidwira ntchito yoti akalalikire uthenga wabwino kwa anthu odulidwa,+
7 Chifukwa cha umboni umenewu,+ ine ndinasankhidwa kuti ndikhale mlaliki ndi mtumwi.+ Ndikunenatu zoona,+ sindikunama ayi. Ndinasankhidwa kuti ndikhale mphunzitsi wophunzitsa anthu a mitundu ina+ za chikhulupiriro+ ndi choonadi.