Aroma 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kudzera mwa iyeyu, tinalandira kukoma mtima+ kwakukulu ndiponso ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti mitundu yonse ikhale yomvera mwa chikhulupiriro+ chifukwa cha dzina lake. Agalatiya 2:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 (pajatu iye amene anapatsa Petulo mphamvu yokhala mtumwi kwa anthu odulidwa ndi amene anapatsanso ine mphamvu+ kuti ndikalalikire kwa anthu a mitundu ina)
5 Kudzera mwa iyeyu, tinalandira kukoma mtima+ kwakukulu ndiponso ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti mitundu yonse ikhale yomvera mwa chikhulupiriro+ chifukwa cha dzina lake.
8 (pajatu iye amene anapatsa Petulo mphamvu yokhala mtumwi kwa anthu odulidwa ndi amene anapatsanso ine mphamvu+ kuti ndikalalikire kwa anthu a mitundu ina)