Machitidwe 9:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli. Aroma 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kudzera mwa iyeyu, tinalandira kukoma mtima+ kwakukulu ndiponso ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti mitundu yonse ikhale yomvera mwa chikhulupiriro+ chifukwa cha dzina lake. Akolose 1:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ineyo ndikugwira ntchito mwakhama kuti ndichite zimenezi, poyesetsa kwambiri+ mogwirizana ndi mphamvu+ yake imenenso ikugwira ntchito mwa ine.+
15 Koma Ambuye anamuuza kuti: “Nyamuka uzipita, chifukwa munthu ameneyu ndi chiwiya changa chochita kusankhidwa+ chotengera dzina langa kupita nalo kwa anthu a mitundu ina,+ komanso kwa mafumu+ ndi ana a Isiraeli.
5 Kudzera mwa iyeyu, tinalandira kukoma mtima+ kwakukulu ndiponso ndinasankhidwa kukhala mtumwi+ kuti mitundu yonse ikhale yomvera mwa chikhulupiriro+ chifukwa cha dzina lake.
29 Ineyo ndikugwira ntchito mwakhama kuti ndichite zimenezi, poyesetsa kwambiri+ mogwirizana ndi mphamvu+ yake imenenso ikugwira ntchito mwa ine.+