Yobu 3:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Limodzi ndi mafumu ndi aphungu a padziko lapansi,+Amene anadzimangira malo omwe tsopano ali bwinja.+ Yesaya 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mafumu ena onse a mitundu ya anthu anagona pansi mu ulemerero, aliyense m’manda ake.+
14 Limodzi ndi mafumu ndi aphungu a padziko lapansi,+Amene anadzimangira malo omwe tsopano ali bwinja.+ Yesaya 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mafumu ena onse a mitundu ya anthu anagona pansi mu ulemerero, aliyense m’manda ake.+