Salimo 92:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti taonani adani anu, inu Yehova!+Adani anu onse adzatha!+Anthu onse ochita zopweteka anzawo adzamwazikana.+ Yohane 8:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chake ndakuuzani kuti, Inu mudzafa m’machimo anu.+ Pakuti ngati simukhulupirira kuti ine ndine amene munali kumuyembekezera uja, mudzafa m’machimo anu.”+
9 Pakuti taonani adani anu, inu Yehova!+Adani anu onse adzatha!+Anthu onse ochita zopweteka anzawo adzamwazikana.+
24 N’chifukwa chake ndakuuzani kuti, Inu mudzafa m’machimo anu.+ Pakuti ngati simukhulupirira kuti ine ndine amene munali kumuyembekezera uja, mudzafa m’machimo anu.”+