Salimo 51:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+ Yesaya 58:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 58 “Fuula mwamphamvu! Usabweze mawu.+ Kweza mawu ako ngati lipenga,+ ndipo uza anthu anga za kupanduka kwawo. A nyumba ya Yakobo uwauze machimo awo.
5 Taonani! Anandilandira mu zowawa za pobereka ndili wochimwa.+Ndipo ndine wochimwa kuchokera pamene mayi anga anatenga pakati panga.+
58 “Fuula mwamphamvu! Usabweze mawu.+ Kweza mawu ako ngati lipenga,+ ndipo uza anthu anga za kupanduka kwawo. A nyumba ya Yakobo uwauze machimo awo.