Yoswa 10:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Yoswa anawapha kuchokera ku Kadesi-barinea+ mpaka ku Gaza+ ndi dera lonse la Goseni+ mpaka ku Gibeoni.+ Oweruza 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako fuko la Yuda linalanda Gaza+ ndi madera ake, Asikeloni+ ndi madera ake ndiponso Ekironi+ ndi madera ake.
41 Yoswa anawapha kuchokera ku Kadesi-barinea+ mpaka ku Gaza+ ndi dera lonse la Goseni+ mpaka ku Gibeoni.+
18 Kenako fuko la Yuda linalanda Gaza+ ndi madera ake, Asikeloni+ ndi madera ake ndiponso Ekironi+ ndi madera ake.