Genesis 10:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa. Deuteronomo 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aavi+ amene anali kukhala m’midzi mpaka kukafika ku Gaza,+ anawonongedwa ndi Akafitori+ ochokera ku Kafitori,+ kuwachotsa pamaso pawo kuti Akafitoriwo akhale m’dzikolo.)
19 Choncho malire a dziko la Akanani anachokera ku Sidoni mpaka ku Gerari+ kufupi ndi Gaza,+ n’kukafika ku Sodomu ndi Gomora+ mpakanso ku Adima+ ndi Zeboyimu,+ kufupi ndi Lasa.
23 Aavi+ amene anali kukhala m’midzi mpaka kukafika ku Gaza,+ anawonongedwa ndi Akafitori+ ochokera ku Kafitori,+ kuwachotsa pamaso pawo kuti Akafitoriwo akhale m’dzikolo.)