-
Machitidwe 27:13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
13 Ndiponso, mphepo ya kum’mwera itayamba kuwomba pang’onopang’ono, anaganiza kuti tsopano zimene anali kufuna zitheka. Choncho anakoka nangula n’kuyamba kuyenda m’mphepete mwa chilumba cha Kerete.
-