Yoswa 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yoswa analanda dziko lonselo, dera lamapiri, dera lonse la Negebu,+ dziko lonse la Goseni,+ ku Sefela,+ ku Araba+ ndiponso dera lamapiri la Isiraeli ndi zigwa zake.+ Yoswa 15:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Goseni,+ Holoni, ndi Gilo.+ Mizinda 11 ndi midzi yake.
16 Yoswa analanda dziko lonselo, dera lamapiri, dera lonse la Negebu,+ dziko lonse la Goseni,+ ku Sefela,+ ku Araba+ ndiponso dera lamapiri la Isiraeli ndi zigwa zake.+